2 Mafumu 15:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Nkhani zina zokhudza Menahemu+ komanso zonse zimene anachita, zinalembedwa mʼbuku la mbiri ya mafumu a Isiraeli.
21 Nkhani zina zokhudza Menahemu+ komanso zonse zimene anachita, zinalembedwa mʼbuku la mbiri ya mafumu a Isiraeli.