2 Mafumu 15:34 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 34 Iye ankachita zoyenera pamaso pa Yehova ngati mmene anachitira bambo ake Uziya.+