-
2 Mafumu 15:36Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
36 Nkhani zina zokhudza Yotamu ndiponso zimene anachita, zinalembedwa mʼbuku la mbiri ya mafumu a Yuda.