2 Mafumu 16:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Kenako Ahazi anachotsa guwa lansembe lakopa*+ limene linali pamaso pa Yehova, kutsogolo kwa nyumbayo. Analichotsa pakati pa guwa lake lansembe ndi nyumba ya Yehova nʼkuliika kumpoto kwa guwa lakelo.
14 Kenako Ahazi anachotsa guwa lansembe lakopa*+ limene linali pamaso pa Yehova, kutsogolo kwa nyumbayo. Analichotsa pakati pa guwa lake lansembe ndi nyumba ya Yehova nʼkuliika kumpoto kwa guwa lakelo.