1 Mbiri 2:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Ana a Yuda anali Ere, Onani ndi Shela. Mwana wamkazi wa Sua wa Chikanani ndi amene anamʼberekera ana atatuwa.+ Koma Ere, mwana woyamba wa Yuda, anachita zoipa pamaso pa Yehova ndipo iye anamupha.+
3 Ana a Yuda anali Ere, Onani ndi Shela. Mwana wamkazi wa Sua wa Chikanani ndi amene anamʼberekera ana atatuwa.+ Koma Ere, mwana woyamba wa Yuda, anachita zoipa pamaso pa Yehova ndipo iye anamupha.+