1 Mbiri 2:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Kenako Hezironi anagona ndi mwana wamkazi wa Makiri+ bambo a Giliyadi.+ Hezironi ali ndi zaka 60, anakwatira mwana wamkazi wa Makiriyo ndipo mkaziyo anamʼberekera Segubu.
21 Kenako Hezironi anagona ndi mwana wamkazi wa Makiri+ bambo a Giliyadi.+ Hezironi ali ndi zaka 60, anakwatira mwana wamkazi wa Makiriyo ndipo mkaziyo anamʼberekera Segubu.