1 Mbiri 2:31 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 31 Mwana* wa Apaimu anali Isi, mwana* wa Isi anali Sesani, mwana* wa Sesani anali Alai.