1 Mbiri 2:46 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 46 Efa, mkazi wamngʼono* wa Kalebe, anabereka Harana, Moza ndi Gazezi. Harana anabereka Gazezi.