-
1 Mbiri 4:10Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
10 Yabezi anapemphera kwa Mulungu wa Isiraeli kuti: “Mundidalitse nʼkukulitsa dera langa ndipo dzanja lanu likhale nane komanso munditeteze ku tsoka kuti lisandivulaze.” Choncho Mulungu anachitadi zimene iye anapempha.
-