1 Mbiri 4:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Meyonatai anabereka Ofira. Seraya anabereka Yowabu bambo a Ge-harasimu,* chifukwa iwo anakhala amisiri.
14 Meyonatai anabereka Ofira. Seraya anabereka Yowabu bambo a Ge-harasimu,* chifukwa iwo anakhala amisiri.