1 Mbiri 4:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Ana a Ezira anali Yeteri, Meredi, Eferi ndi Yaloni. Mkaziyo* anatenga pakati nʼkubereka Miriamu, Samai ndi Isiba bambo a Esitemowa.
17 Ana a Ezira anali Yeteri, Meredi, Eferi ndi Yaloni. Mkaziyo* anatenga pakati nʼkubereka Miriamu, Samai ndi Isiba bambo a Esitemowa.