1 Mbiri 4:27 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 Simeyi anali ndi ana aamuna 16 aakazi 6, koma azichimwene ake analibe ana ambiri. Pa mabanja awo panalibe banja limene linali ndi ana ambiri ngati mabanja a Ayuda.+
27 Simeyi anali ndi ana aamuna 16 aakazi 6, koma azichimwene ake analibe ana ambiri. Pa mabanja awo panalibe banja limene linali ndi ana ambiri ngati mabanja a Ayuda.+