1 Mbiri 4:40 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 40 Kenako anapeza msipu wabwino kwambiri ndipo dera lake linali lalikulu ndiponso lopanda chosokoneza chilichonse. Anthu amene ankakhala kumeneko kale anali mbadwa za Hamu.+
40 Kenako anapeza msipu wabwino kwambiri ndipo dera lake linali lalikulu ndiponso lopanda chosokoneza chilichonse. Anthu amene ankakhala kumeneko kale anali mbadwa za Hamu.+