1 Mbiri 5:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 ndi Bela. Bela anali mwana wa Azazi, Azazi anali mwana wa Sema, Sema anali mwana wa Yoweli. Bela ankakhala mʼdera loyambira ku Aroweli+ mpaka kukafika ku Nebo ndi ku Baala-meoni.+
8 ndi Bela. Bela anali mwana wa Azazi, Azazi anali mwana wa Sema, Sema anali mwana wa Yoweli. Bela ankakhala mʼdera loyambira ku Aroweli+ mpaka kukafika ku Nebo ndi ku Baala-meoni.+