-
1 Mbiri 5:10Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
10 Mʼmasiku a Sauli, iwo anamenyana ndi mbadwa za Hagara nʼkuzigonjetsa. Kenako anayamba kukhala mʼmahema awo mʼdera lonse lakumʼmawa kwa Giliyadi.
-