-
1 Mbiri 5:14Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
14 Amenewa anali ana a Abihaili. Abihaili anali mwana wa Huri, Huri anali mwana wa Yarowa, Yarowa anali mwana wa Giliyadi, Giliyadi anali mwana wa Mikayeli, Mikayeli anali mwana wa Yesisai, Yesisai anali mwana wa Yado ndipo Yado anali mwana wa Buza.
-