1 Mbiri 5:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Iwo ankakhala ku Giliyadi,+ ku Basana+ ndi mʼmidzi yozungulira komanso mʼmalo onse odyetsera ziweto a ku Sharoni, mpaka kumapeto kwa malo amenewa.
16 Iwo ankakhala ku Giliyadi,+ ku Basana+ ndi mʼmidzi yozungulira komanso mʼmalo onse odyetsera ziweto a ku Sharoni, mpaka kumapeto kwa malo amenewa.