1 Mbiri 5:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Onsewa analembedwa pamndandanda wa mayina wotsatira makolo awo, mʼmasiku a Yotamu+ mfumu ya Yuda ndi mʼmasiku a Yerobowamu*+ mfumu ya Isiraeli.
17 Onsewa analembedwa pamndandanda wa mayina wotsatira makolo awo, mʼmasiku a Yotamu+ mfumu ya Yuda ndi mʼmasiku a Yerobowamu*+ mfumu ya Isiraeli.