1 Mbiri 5:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Anthu a hafu ya fuko la Manase+ ankakhala kuyambira ku Basana mpaka ku Baala-herimoni, ku Seniri ndi kuphiri la Herimoni+ ndipo anachuluka kwambiri.
23 Anthu a hafu ya fuko la Manase+ ankakhala kuyambira ku Basana mpaka ku Baala-herimoni, ku Seniri ndi kuphiri la Herimoni+ ndipo anachuluka kwambiri.