1 Mbiri 5:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 Koma iwo anachita zinthu zosakhulupirika kwa Mulungu wa makolo awo ndipo anachita chiwerewere ndi milungu ya anthu amʼdzikolo,+ amene Mulungu anawapha pamaso pawo.
25 Koma iwo anachita zinthu zosakhulupirika kwa Mulungu wa makolo awo ndipo anachita chiwerewere ndi milungu ya anthu amʼdzikolo,+ amene Mulungu anawapha pamaso pawo.