1 Mbiri 6:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Mwana wa Gerisomu+ anali Libini, mwana wa Libini anali Yahati, mwana wa Yahati anali Zima,