1 Mbiri 6:32 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 32 Anthuwa ankayangʼanira oimba pachihema chopatulika kapena kuti chihema chokumanako, mpaka pamene Solomo anamanga nyumba ya Yehova ku Yerusalemu.+ Iwo ankatumikira mogwirizana ndi ntchito yomwe anapatsidwa.+
32 Anthuwa ankayangʼanira oimba pachihema chopatulika kapena kuti chihema chokumanako, mpaka pamene Solomo anamanga nyumba ya Yehova ku Yerusalemu.+ Iwo ankatumikira mogwirizana ndi ntchito yomwe anapatsidwa.+