-
1 Mbiri 6:54Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
54 Malo otsatirawa ndi amene mbadwa za Aroni za kubanja la Kohati zinkakhala mʼmadera awo komanso mʼmisasa yawo yokhala ndi mipanda, chifukwa maere oyamba anagwera iwowo:
-