1 Mbiri 6:61 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 61 Atachita maere, anthu a mʼbanja la Kohati amene anatsala anawapatsa mizinda yochokera ku banja la fuko lina ndi hafu ya fuko la Manase.+ Anawapatsa mizinda 10.
61 Atachita maere, anthu a mʼbanja la Kohati amene anatsala anawapatsa mizinda yochokera ku banja la fuko lina ndi hafu ya fuko la Manase.+ Anawapatsa mizinda 10.