-
1 Mbiri 6:70Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
70 Kuchokera ku hafu ya fuko la Manase, anapatsa mabanja a Kohati amene anatsala, mzinda wa Aneri ndi malo ake odyetserako ziweto ndiponso mzinda wa Bileamu ndi malo ake odyetserako ziweto.
-