-
1 Mbiri 7:2Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
2 Ana a Tola anali Uzi, Refaya, Yerieli, Yahamai, Ibisamu ndi Semuyeli. Amenewa anali atsogoleri a nyumba za makolo awo. Pa mbadwa za Tola panali asilikali amphamvu ndipo mʼmasiku a Davide, asilikaliwa analipo 22,600.
-