-
1 Mbiri 7:4Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
4 Pa mbadwa za anthu amenewa, motsatira nyumba za makolo awo, panali asilikali okonzeka kumenya nkhondo okwana 36,000, chifukwa anali ndi akazi ndi ana ambiri.
-