1 Mbiri 7:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Abale awo a mabanja onse a Isakara, anali asilikali amphamvu okwana 87,000 pamndandanda wa mayina awo wotsatira makolo awo.+
5 Abale awo a mabanja onse a Isakara, anali asilikali amphamvu okwana 87,000 pamndandanda wa mayina awo wotsatira makolo awo.+