1 Mbiri 7:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Ana a Bela analipo 5: Eziboni, Uzi, Uziyeli, Yerimoti ndi Iri. Iwo anali atsogoleri a nyumba za makolo awo, asilikali amphamvu ndipo pamndandanda wa mayina wotsatira makolo awo, analipo 22,034.+
7 Ana a Bela analipo 5: Eziboni, Uzi, Uziyeli, Yerimoti ndi Iri. Iwo anali atsogoleri a nyumba za makolo awo, asilikali amphamvu ndipo pamndandanda wa mayina wotsatira makolo awo, analipo 22,034.+