1 Mbiri 7:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Ana a Nafitali+ anali Yazieli, Guni, Yezera ndi Salumu ndipo anali mbadwa za Biliha.+