1 Mbiri 7:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Tahati anabereka Zabadi ndipo Zabadi anabereka Sutela. Efuraimu anaberekanso Ezeri ndi Eleadi. Iwo anaphedwa ndi anthu a ku Gati+ amene anabadwira mʼdzikolo, chifukwa anapita kukatenga ziweto zawo.
21 Tahati anabereka Zabadi ndipo Zabadi anabereka Sutela. Efuraimu anaberekanso Ezeri ndi Eleadi. Iwo anaphedwa ndi anthu a ku Gati+ amene anabadwira mʼdzikolo, chifukwa anapita kukatenga ziweto zawo.