1 Mbiri 7:40 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 40 Onsewa anali ana a Aseri, atsogoleri a nyumba za makolo awo, asilikali amphamvu ochita kusankhidwa. Iwo anali akuluakulu a atsogoleri ndipo pamndandanda wa mayina awo wotsatira makolo awo+ analipo amuna 26,000+ okonzeka kumenya nkhondo.
40 Onsewa anali ana a Aseri, atsogoleri a nyumba za makolo awo, asilikali amphamvu ochita kusankhidwa. Iwo anali akuluakulu a atsogoleri ndipo pamndandanda wa mayina awo wotsatira makolo awo+ analipo amuna 26,000+ okonzeka kumenya nkhondo.