-
1 Mbiri 8:40Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
40 Ana a Ulamu anali asilikali amphamvu amuna odziwa kugwira uta. Iwo anali ndi ana ambiri ndiponso zidzukulu zambiri. Onse analipo 150. Onsewa anali mbadwa za Benjamini.
-