1 Mbiri 9:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Ndipo mbadwa zina za Yuda,+ za Benjamini,+ za Efuraimu ndi za Manase zinkakhala ku Yerusalemu.