1 Mbiri 9:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Pa mbadwazi panali Utai mwana wa Amihudi. Amihudi anali mwana wa Omuri, Omuri anali mwana wa Imiri ndipo Imiri anali mwana wa Bani. Amenewa anali mbadwa za Perezi+ mwana wa Yuda.
4 Pa mbadwazi panali Utai mwana wa Amihudi. Amihudi anali mwana wa Omuri, Omuri anali mwana wa Imiri ndipo Imiri anali mwana wa Bani. Amenewa anali mbadwa za Perezi+ mwana wa Yuda.