-
1 Mbiri 9:8Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
8 Panalinso Ibineya mwana wa Yerohamu ndi Ela mwana wa Uzi ndipo Uzi anali mwana wa Mikiri. Komanso panali Mesulamu mwana wa Sefatiya. Sefatiya anali mwana wa Reueli ndipo Reueli anali mwana wa Ibiniya.
-