-
1 Mbiri 9:13Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
13 Panalinso abale awo. Onse anali atsogoleri a nyumba ya makolo awo ndipo analipo 1,760. Iwo anali amuna amphamvu ndiponso oyenerera, omwe ankatumikira panyumba ya Mulungu woona.
-