1 Mbiri 9:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Pagulu la Alevi panali Semaya+ mwana wa Hasubu. Hasubu anali mwana wa Azirikamu ndipo Azirikamu anali mwana wa Hasabiya. Amenewa anali mbadwa za Merari.
14 Pagulu la Alevi panali Semaya+ mwana wa Hasubu. Hasubu anali mwana wa Azirikamu ndipo Azirikamu anali mwana wa Hasabiya. Amenewa anali mbadwa za Merari.