1 Mbiri 9:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Komanso panali Obadiya mwana wa Semaya. Semaya anali mwana wa Galali, Galali anali mwana wa Yedutuni. Ndiye panalinso Berekiya mwana wa Asa mwana wa Elikana, amene ankakhala mʼmidzi ya Anetofa.+
16 Komanso panali Obadiya mwana wa Semaya. Semaya anali mwana wa Galali, Galali anali mwana wa Yedutuni. Ndiye panalinso Berekiya mwana wa Asa mwana wa Elikana, amene ankakhala mʼmidzi ya Anetofa.+