1 Mbiri 9:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Zekariya+ mwana wa Meselemiya anali mlonda wapageti lolowera kuchihema chokumanako.