1 Mbiri 9:28 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 28 Ena a iwo ankayangʼanira ziwiya+ zogwiritsa ntchito pa utumiki ndipo ankaziwerenga pozitulutsa ndi pozilowetsa.
28 Ena a iwo ankayangʼanira ziwiya+ zogwiritsa ntchito pa utumiki ndipo ankaziwerenga pozitulutsa ndi pozilowetsa.