1 Mbiri 9:31 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 31 Matitiya Mlevi, yemwe anali mwana woyamba wa Salumu mbadwa ya Kora, anali ndi udindo woyangʼanira zinthu zophikidwa mʼziwaya,+ umene anapatsidwa chifukwa cha kukhulupirika kwake.
31 Matitiya Mlevi, yemwe anali mwana woyamba wa Salumu mbadwa ya Kora, anali ndi udindo woyangʼanira zinthu zophikidwa mʼziwaya,+ umene anapatsidwa chifukwa cha kukhulupirika kwake.