1 Mbiri 11:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Anthu a ku Yebusi anayamba kunyoza Davide kuti: “Sudzalowa mumzinda uno.”+ Koma Davide analanda malo amene anali mumpanda wolimba kwambiri mu Ziyoni,+ umene panopa ndi Mzinda wa Davide.+
5 Anthu a ku Yebusi anayamba kunyoza Davide kuti: “Sudzalowa mumzinda uno.”+ Koma Davide analanda malo amene anali mumpanda wolimba kwambiri mu Ziyoni,+ umene panopa ndi Mzinda wa Davide.+