1 Mbiri 11:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Kenako Davide anayamba kumanga mzinda pamalo onsewo, kuyambira ku Chimulu cha Dothi* mpaka kumadera ozungulira, ndipo Yowabu ndi amene anamalizitsa kumanga mzindawo.
8 Kenako Davide anayamba kumanga mzinda pamalo onsewo, kuyambira ku Chimulu cha Dothi* mpaka kumadera ozungulira, ndipo Yowabu ndi amene anamalizitsa kumanga mzindawo.