-
1 Mbiri 11:18Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
18 Atatero amuna atatu aja analimbana ndi anthu mpaka kulowa mumsasa wa Afilisiti nʼkukatunga madzi mʼchitsime chimene chinali pageti la ku Betelehemu ndipo anapita nawo kwa Davide. Koma iye anakana kumwa madziwo. Mʼmalomwake anawapereka kwa Yehova powathira pansi.
-