1 Mbiri 12:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Amuna amenewa anali onyamula mauta ndipo ankatha kugwiritsa ntchito mkono wamanja ndi wamanzere+ poponya miyala ndi gulaye+ kapena poponya mivi ndi uta. Amenewa anali abale ake a Sauli, a fuko la Benjamini.+
2 Amuna amenewa anali onyamula mauta ndipo ankatha kugwiritsa ntchito mkono wamanja ndi wamanzere+ poponya miyala ndi gulaye+ kapena poponya mivi ndi uta. Amenewa anali abale ake a Sauli, a fuko la Benjamini.+