1 Mbiri 12:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Davide atapita ku Zikilaga,+ anthu ena a fuko la Manase anapita kumbali yake. Anthuwo anali Adinala, Yozabadi, Yediyaeli, Mikayeli, Yozabadi, Elihu ndi Ziletai. Aliyense anali mtsogoleri wa asilikali 1,000, a fuko la Manase.+
20 Davide atapita ku Zikilaga,+ anthu ena a fuko la Manase anapita kumbali yake. Anthuwo anali Adinala, Yozabadi, Yediyaeli, Mikayeli, Yozabadi, Elihu ndi Ziletai. Aliyense anali mtsogoleri wa asilikali 1,000, a fuko la Manase.+