-
1 Mbiri 13:2Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
2 Kenako anauza gulu lonse la Isiraeli kuti: “Ngati mukuona kuti ndi bwino ndiponso ngati zili zovomerezeka kwa Yehova Mulungu wathu, tiyeni titumize uthenga kwa abale athu mʼmadera onse a Isiraeli. Uthengawu upitenso kwa ansembe ndi Alevi mʼmizinda yawo yonse+ yokhala ndi malo odyetserako ziweto, kuti abwere kuno.
-