1 Mbiri 13:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Davide ndi Aisiraeli onse anapita ku Baala,+ ku Kiriyati-yearimu, amene ali mʼdera la Yuda kukatenga Likasa la Mulungu woona, Yehova, amene amakhala pamwamba* pa akerubi.+ Pa Likasa limeneli, anthu amaitanirapo dzina lake.
6 Davide ndi Aisiraeli onse anapita ku Baala,+ ku Kiriyati-yearimu, amene ali mʼdera la Yuda kukatenga Likasa la Mulungu woona, Yehova, amene amakhala pamwamba* pa akerubi.+ Pa Likasa limeneli, anthu amaitanirapo dzina lake.