1 Mbiri 13:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Davide ndi Aisiraeli onse ankasangalala kwambiri pamaso pa Mulungu woona. Iwo ankaimba nyimbo ndi azeze, zoimbira zina za zingwe, maseche,+ zinganga+ ndi malipenga.+
8 Davide ndi Aisiraeli onse ankasangalala kwambiri pamaso pa Mulungu woona. Iwo ankaimba nyimbo ndi azeze, zoimbira zina za zingwe, maseche,+ zinganga+ ndi malipenga.+